Song parody of

Yekha

by JEG Tellem

Here's where you get creative! Use our cool song parody creator to make a totally new musical idea and lyrics for the Yekha song by JEG Tellem.

Simply click on any word to get rhyming words suggestion to use instead of the original ones. You may also remove or alter entire lines if needed — when you're done save your work and share it with our community — have fun!

  • English (English)
  • Français (French)
  • Español (Spanish)

ye ye yeee yeeeh oh Yeeeh Tellem aha Yeah here we go Ndimafunitsitsa nditakhala wabwino Aliyense atamatengela ine Ndimafunitsitsa nditakhala chitsanzo Cholozeka pagulu la anthu Koma nthawi zambiri Ndimagwetsedwa Mphwayi Chifukwa Cha zinthu zondizungulila Ndati nthawi zambiri Ndimabwezedwa mbuyo Chifukwa Cha zochita za anthu ena Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi (Izi) Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Ndimafuna Njira zanga utasintha Ndimafuna Koma zimandikanika Ndimafuna Ndimafuna kukomana Ndimamuna Mamuna wa mtanda koma Koma ndikazamva za abusa Awapezelela ndi sister NKHANI ija ayiphiphilitsa Ine sizimandilimbikitsa ehe Ndikaona zophinja Sindichedwa ine kugiva Sindisilila u beliver Ndimaona ngati ndichedwa ehe Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Moyo wanga aha Njira zanga izi Ndimafuna zizikhala za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi Ndimafuna ndizichita za Yehova yekha Moyo wanga aha Njira zanga izi za Yehova yekha Thupi langa aha Ntchito zanga izi za Yehova yekha Za Yehova yekha za Yehova yekha Zizikhala za Yehova yekha Za Yehova yekha za Yehova yekha Iye Yesu

Done creating your parody?

Don't keep it to yourself! Save it now so you can share it with the rest of the world!

Watch the song video

Yekha

2
0     0

Browse Lyrics.com

Quiz

Are you a music master?

»
Which group sang the song "96 Tears"?
A Count Five
B The Sonics
C Paul Revere and the Raidersr9
D Question Mark and the Mysterians

Free, no signup required:

Add to Chrome

Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

Free, no signup required:

Add to Firefox

Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!

JEG Tellem tracks

On Radio Right Now

Loading...

Powered by OnRad.io


Think you know music? Test your MusicIQ here!