Song parody of

Ponya

by Tha HP

Here's where you get creative! Use our cool song parody creator to make a totally new musical idea and lyrics for the Ponya song by Tha HP.

Simply click on any word to get rhyming words suggestion to use instead of the original ones. You may also remove or alter entire lines if needed — when you're done save your work and share it with our community — have fun!

  • English (English)
  • Français (French)
  • Español (Spanish)

Mwina ndikaponya Mbedza yangayi sindikola Mwinamwake sin'dziwa kuwedza Ndeno chinachake chindiletsa Mwina ndikaponya Mwala wangawu sukawomba Chinachake mtima chindilasa Mwinamwake sin'dziwa kusaka Mwina ndika-- Shatapu iwe ponya Zoti sungathe sudziwa ponya Usazibweze ndikukayikira ponya Ungathe sungathe sungadziwe pokhapokha upange chisankho, ponya Zoti sungathe sudziwa ponya Usazibweze ndikukayikira ponya Ungathe sungathe sungadziwe pokhapokha utaponya Tonse timaopa Mantha akabwera anthu timafooka Mtima okayika umazatikoka Kufuna kutichotsera zomwe timalota (Koma osafooka) Koma osafooka Kutsogolo kuli kuwala kokhakokha Bola chikayiko chako utachotsa 'Mwinamwake ine sin'ziwa kutosa,' mphwayiyo ndi tsoka Khala chete ponya Zoti sungathe sudziwa ponya Usazibweze ndikukayikira ponya Ungathe sungathe sungadziwe pokhapokha upange chisankho, ponya Zoti sungathe sudziwa ponya Usazibweze ndikukayikira ponya Ungathe sungathe sungadziwe pokhapokha utaponya

Done creating your parody?

Don't keep it to yourself! Save it now so you can share it with the rest of the world!

Browse Lyrics.com

Quiz

Are you a music master?

»
Finish the Johnny Cash line. "Mr. Garfield's been ____."
A caught in a lie
B to Oklahoma
C shot down low
D eatin' biscuits and bacon

Free, no signup required:

Add to Chrome

Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

Free, no signup required:

Add to Firefox

Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!

Tha HP tracks

On Radio Right Now

Loading...

Powered by OnRad.io


Think you know music? Test your MusicIQ here!