SHANDANGUZA (feat. LazyB)
JEG Tellem
The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com
Kukunokulilongwe Osaiwala, pompaja, a Lazy again Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Mungogona, mungokoka guza Mukula mopusa Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Ana ogona Mungokoka guza Mukula mopusa Ngati GABA JEG tandipase shotitu Kwathu ndi kutalika koma JEG ndi shotitu Sindifila gin koma ndimenyabe shotitu Ndimatha kupha beat kuombela zima shotitu Chi mento chili mwala lazy b achiponde Sine mwana okulila chiponde Zaine funsa Steve Chinga mofat Muvu yanga sia nkhumba yachi more fat ANangovela GABA mtima wao gugugu Nangovaya ngati Eli hit ya gugugu Ine ndinali zoba ku past tu Pano ndilibe two koloko ndi past two Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Mungogona, mungokoka guza Mukula mopusa Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Ana ogona Mungokoka guza Mukula mopusa Mfana wamfupi kuno ku Lilongwe Ndithoke ngamo ati ndi chipongwe Ndili pa level 4 inu nti mabongwe Musakambe za beef mukudya bonongwe Olo mdima ugwe Magetsi ngwe Ndife ana achikoka popanda zingwe Mbili inaenda yokha, mpaka ku mpingwe Amanditcha Mr. Short guy ine ndi igwe They call me big man, big shot The Don D D I do run Big things with profit Ku two far Fourner the whole city Sick man, ine ndi covid Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Mungogona, mungokoka guza Mukula mopusa Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Ana ogona Mungokoka guza Mukula mopusa ANangovela GABA mtima wao gugugu Nangovaya ngati Eli hit ya gugugu Ine ndinali zoba ku past tu Pano ndilibe two koloko ndi past two They call me big man, big shot The Don D D I do run Big things with profit Ku two far Fourner the whole city Sick man, ine ndi covid Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Mungogona, mungokoka guza Mukula mopusa Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Ana ogona Mungokoka guza Mukula mopusa Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Mungogona, mungokoka guza Mukula mopusa Ndangobwela, kuza shandanguza Ndikupusha, ndikugadabuza Ana ogona Mungokoka guza Mukula mopusa
Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"SHANDANGUZA (feat. LazyB) Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 3 Jun 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/14258537/JEG+Tellem/SHANDANGUZA+%28feat.+LazyB%29>.
Discuss the SHANDANGUZA (feat. LazyB) Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In