Basics

T-No

0 fans

T-No


3:46

 The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com

Yeah, Sibabaze yeah...

Nde pali ma guys ena ake amati TNO... Kodi utulutsa single ina liti

I'm like... I'm working on the basics so...
Let me tell me what I'm talking about... You need to do this too... Listen...

Wake up and I praise God
Glad I got see another day
It aint luck it's a blessing Praising God is a basic
Hit the floor with knees huh
Say a prayer for you leave huh God be with me please huh Kupemphera ndi ma basic
Flip a page through the bible I'm a Jesus' disciple
That's my ammo and my rifle
Daily bread is a basic 
Meditate on the scriptures hearing God when he whispers 
Sharing whatever he teach us Evangelism is a basic
Kufalitsa mawu (Yeah, yeah)
Kupantha uthenga (Yeah, yeah) Wa Namalenga (Yeah, yeah)
Kulalikira ndi ma basic
Kukonda anzako monga iwenso osakondera (Yeah, yeah)
Osalephera (Yeah, yeah), Amenewonso ndi ma basic
Ndikufunika kuti, ndisayiwale maziko athu
Pali zingapo
Zomwe zimafunikatu 
Monga Mchristu
Pali ziwiri zitatu
Zomwe ndufunika kuti ndisayiwale ndizichitatu (Yeah yeah)

Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic
Daily bread is a basic
All of these are basics Evangelism is a basic
Kulalikira ndi ma basic
Kukonda anzako ma basic
Amenewonso ndi ma basic
Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic
Daily bread is a basic
All of these are basics Evangelism is a basic
Kulalikira ndi ma basic
Kukonda anzako ma basic
Amenewonso ndi ma basic

Be a giver that's a basic
It's more blessed than receiving
Not because you wanna get more
But you want to make a difference
Wanna be a legend be a giver, everybody know that's a basic
Wanna be a leader, be a servant everybody know that's a basic
Kulemekeza abambo ndi amayi ako omwetu ndi ma basic
Kupereka ulemu kwa munthu wamkulu kuposa iwe ndi basic
Kukhala chete ndikumvetsera kaye usanayankhule ndi basic
Ndiye chonde osapala
Tsatanikoni ma basic
Kupita ktchalitchi muzitengakotu bayibulotu ndi basic
Kuyamba chibwenzi muzikhala kuti mwapemphera kaye ndi basic
Osavutitsa mwana wa nzanu musanakonzeke ndi basic
Osayamba zinthu popanda plan amenewa ndi ma basic
Ndikufunika kuti, ndisayiwale maziko athu
Pali zingapo
Zomwe zimafunikatu 
Monga Mchristu
Pali ziwiri zitatu
Zomwe ndufunika kuti ndisayiwale ndizichitatu (Yeah yeah)

Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic
Daily bread is a basic
All of these are basics Evangelism is a basic
Kulalikira ndi ma basic
Kukonda anzako ma basic
Amenewonso ndi ma basic

Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic
Daily bread is a basic
All of these are basics Evangelism is a basic
Kulalikira ndi ma basic
Kukonda anzako ma basic
Amenewonso ndi ma basic
Praising God is a basic Kupemphera ndi ma basic
Daily bread is a basic
All of these are basics Evangelism is a basic
Kulalikira ndi ma basic
Kukonda anzako ma basic
Amenewonso ndi ma basic

 The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com

Written by: Edward Chikhwenda

Lyrics © DistroKid

Lyrics Licensed & Provided by LyricFind

Discuss the Basics Lyrics with the community:

0 Comments

    Citation

    Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:

    Style:MLAChicagoAPA

    "Basics Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 29 Apr. 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/3847627/T-No/Basics>.

    Missing lyrics by T-No?

    Know any other songs by T-No? Don't keep it to yourself!

    Browse Lyrics.com

    Quiz

    Are you a music master?

    »
    The name of the singer known as "Swae Lee" is?
    A Khalif Malik Ibn Shaman Brown
    B William Lee Ellis
    C Jon Peter Lewis
    D Jeffrey Lee Pierce

    Free, no signup required:

    Add to Chrome

    Get instant explanation for any lyrics that hits you anywhere on the web!

    Free, no signup required:

    Add to Firefox

    Get instant explanation for any acronym or abbreviation that hits you anywhere on the web!

    T-No tracks

    On Radio Right Now

    Loading...

    Powered by OnRad.io


    Think you know music? Test your MusicIQ here!