Panado
Onesimus
Become A Better Singer In Only 30 Days, With Easy Video Lessons!
Panado panado yeah mmm ma headache yeah mmm eeh Panado panado mmm eeh Amakonda miseche Amakondwa munthu adzivutika Zochitika ngati siopemphera Daily daily busy ntopola Kubaya ma damage Kuupasa moyo wanga challenge Machitidwe awo ngati Judas Makhalidwe awo ngati njenjete eeh Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Ndi nsanje apatseni, panado panado Panado panado Amweko panado panado Panado anado Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka mwina ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega Samafuna ndiyendere njale Samakondwa ndikamadya money Zikandiyendera amakoka chibale Zikamandivuta andinyoza kumbali Koma mulungu andichita balance, I relax Amamenya nkhondo nditakhala pansi Adani anga onse alemba m’madzi Samakondwa nane Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Amafuna ndikokoloke Amakhumbira nditaphokoloka Amafuna ndisokoloke Amafuna mwina nditakomoka Ndi nsanje apatseni, panado panado Panado panado Amweko panado panado Panado panado Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka mwina ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega Mutu wakula ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka ndi nsanje Kaduka, mtima wachigawega
The easy, fast & fun way to learn how to sing: 30DaySinger.com
Written by: Armstrong Kalua, Mphatso Nancginga
Lyrics © DistroKid
Lyrics Licensed & Provided by LyricFind
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"Panado Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 8 Jun 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/5258246/Onesimus/Panado>.
Discuss the Panado Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In