Vuto
Ritaa
Struggling with Vuto? Become a better singer in 30 days with these videos!
Nkhawa yandigwira (I am stressed) Mnyumba mwa anzanga, ana Mpaka akula (In my mates houses, the children are grown) Chomwe ndingamange, chingomasuka (What I tie, gets untied) Ndingaumbe, chingogumuka (What I make, it breaks Ndingatole, chingotaika (What I pick, it drops) Anthu akundiseka ine (They are laughing at me Akuti undisiya ine (They say you'll leave me) Upeza wina iwe (You'll find another) Anthu akundiseka ine (They are laughing at me) Akuti undisiya ine (They say you'll leave me) Upeza wina iwe (You'll find another) Mwina vuto ndi ine (Maybe I am the problem) Vuto ndi ine, vuto ndi ine Vuto ndi ine, vuto ndi ine Amati akulu ndiye m'dambo (They say elders are a pond) Mozimira moto (That quenches fires) Ndipatseni malangizo (Tell me what to do) Mukuti yesabe, yesabe (You say keep trying) Komabe, komabe (But still, but still) Chitonzo changa chagwera pa mwana (My problem is a child) Anthu akundiseka ine (They are laughing at me Akuti undisiya ine (They say you'll leave me) Upeza wina iwe (You'll find another) Anthu akundiseka ine (They are laughing at me) Akuti undisiya ine (They say you'll leave me) Upeza wina iwe (You'll find another) Mwina vuto ndi ine (Maybe I am the problem) Vuto ndi ine, Vuto ndi ine Vuto ndi ine, Vuto ndi ine Mwina vuto si ine (But maybe I am not the problem) Hey (But maybe Iam not the problem)
Watch: New Singing Lesson Videos Can Make Anyone A Great Singer
Citation
Use the citation below to add these lyrics to your bibliography:
Style:MLAChicagoAPA
"Vuto Lyrics." Lyrics.com. STANDS4 LLC, 2024. Web. 7 May 2024. <https://www.lyrics.com/lyric-lf/7660173/Ritaa/Vuto>.
Discuss the Vuto Lyrics with the community:
Report Comment
We're doing our best to make sure our content is useful, accurate and safe.
If by any chance you spot an inappropriate comment while navigating through our website please use this form to let us know, and we'll take care of it shortly.
Attachment
You need to be logged in to favorite.
Log In